Sitigawana (Edit)

歌词
混音师 : Greg Freeman/Rudimental/The Martinez Brothers
音频工程师 : Conor Bellis
合成器 : Piers Aggett
吉他 : Amir Amor
鼓编程 : Amir Amor/Chris Martinez/Kesi Dryden/Leon Rolle/Piers Aggett/Steven Martinez
母带工程师 : Kevin Grainger
Rudimental 、The Martinez Brothers 、Faith Mussa -Sitigawana (Edit)
Aphiri anabwera kuchoka ku harare
Aphiri anabwera kuchoka ku harare
Koma nkati mwa sutekesi munalibe kanthu shuwa
Koma nkati mwa sutekesi munalibe kanthu shuwa
Aphiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti
Makolo anga onse anamwalira ku dara
Aphiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti
Makolo anga onse anamwalira ku dara
Koma nkati mwa sutekesi munalibe kanthu shuwa
Koma nkati mwa sutekesi munalibe kanthu shuwa
Aphiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti
Makolo anga onse anamwalira ku dara
Aphiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti
Makolo anga onse anamwalira ku dara
Oh sitigawana
Oh sitigawana sitigawana
Oh sitigawana zida
Anamwalira ku dara
Anamwalira ku dara
Oh sitigawana zida
Sitigawana
Sitigawana zida
Sitigawana
Sitigawana
Sitigawana
Oh sitigawana zida
Sitigawana
Sitigawana
Oh sitigawana zida
Anamwalira ku dara
Anamwalira ku dara
Sitigawana zida
Sitigawana
Sitigawana
Oh sitigawana zida
Anamwalira ku dara
Anamwalira ku dara
Anamwalira ku dara
Koma nkati mwa sutekesi munalibe kanthu shuwa
Koma nkati mwa sutekesi munalibe kanthu shuwa
Aphiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti
Makolo anga onse anamwalira ku dara
Aphiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti
Makolo anga onse anamwalira ku dara
专辑信息
1.Sitigawana (Edit)
2.Sitigawana